| Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife? | |
Mmene Mungagwiritsire Ntchito Brosha Lino |
|
Brosha lino lakonzedwa monga kosi yophunzira Baibulo. Kodi liyenera kugwiritsiridwa ntchito motani? Tikupereka njira yotsatirayi: Kuchiyambi kwa phunziro lililonse, kuli mafunso. M’mabulaketi otsatira funso lililonse, mudzapezamo manambala a ndime zimene mayankho akupezekamo. Ŵerengani mafunsowo choyamba. Asinkhesinkheni. Ndiyeno ŵerengani ndime iliyonse, ndi kuŵerenga malemba ake m’Baibulo lanu. Mutamaliza phunzirolo, pitaninso ku mafunso ndi kuyesa kukumbukira yankho la Baibulo pafunso lililonse. Mutamaliza brosha lonse, bwereranimo m’mafunso onse. |
Kofalitsidwa mu 1996 |
|
Copyright © 2008 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. All rights reserved. |
|